13 Uzikanenatu, kuti iwe ndiwe mlongo wanga: kuti cidzakhala cabwino ndi ine, cifukwa ca iwe, ndi kuti moyo wanga usungike ndi iwe.
Werengani mutu wathunthu Genesis 12
Onani Genesis 12:13 nkhani