16 Ndipo ndidzayesa mbeu yako monga pfumbi lapansi: cotere kuti ngati munthu angathe kuwerenga pfumbi lapansi, comweconso mbeu yako idzawerengedwa.
Werengani mutu wathunthu Genesis 13
Onani Genesis 13:16 nkhani