10 Cigwa ca Sidimu cinali ndi zitengetenge tho; ndipo anathawa mafumu a ku Sodomu ndi Gomora nagwa m'menemo: amene anatsala anathawira kuphiri.
Werengani mutu wathunthu Genesis 14
Onani Genesis 14:10 nkhani