Genesis 14:15 BL92

15 Ndipo anadzigawanizira iwo usiku, iye ndi anyamata ace, nawakantha, nawapitikitsa kufikira ku Hoba, ndiko ku dzanja lamanzere la ku Damasiko.

Werengani mutu wathunthu Genesis 14

Onani Genesis 14:15 nkhani