1 Zitapita izo, mau a Yehova anadza kwa Abramu m'masomphenya, kuti, Usaope, Abramu, Ine ndine cikopa cako ndi mphotho yako yaikurukuru.
Werengani mutu wathunthu Genesis 15
Onani Genesis 15:1 nkhani