Genesis 15:13 BL92

13 Ndipo anati kwa Abramu, Dziwitsa ndithu kuti mbeu zako zidzakhala alendo m'dziko la eni, nizidzatumikira iwo, ndipo iwo adzasautsa izo zaka mazana anai;

Werengani mutu wathunthu Genesis 15

Onani Genesis 15:13 nkhani