Genesis 16:16 BL92

16 Ndipo Abramu anali wa zaka makumi asanu ndi atatu kudza zisanu ndi cimodzi, pamene Hagara anambalira Abramu Ismayeli.

Werengani mutu wathunthu Genesis 16

Onani Genesis 16:16 nkhani