Genesis 17:27 BL92

27 Ndipo amuna onse a m'nyumba mwace obadwa m'nyumba, ndi ogulidwa ndi ndalama kwa alendo, anadulidwa pamodzi naye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 17

Onani Genesis 17:27 nkhani