Genesis 18:10 BL92

10 Ndipo anati, Ndidzabwera kwa iwe ndithu pakufika nyengo yace; taonani Sara mkazi wako adzakhala ndi mwana wamwamuna. Ndipo Sara anamva pakhomo pa hema amene anali pambuyo pace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 18

Onani Genesis 18:10 nkhani