28 kapena akaperewera asanu pa olungama makumi asanuwo; kodi mudzaononga mudzi wonse cifukwa ca kuperewera asanu? Ndipo anati, Ndikapeza makumi anai ndi asanu sindidzauononga.
Werengani mutu wathunthu Genesis 18
Onani Genesis 18:28 nkhani