5 ndipo ndidzatenga cakudya pang'ono, nimutonthoze mitima yanu; mutatero mudzapitirira, cifukwa mwafika kwa kapolo wanu. Ndipo anati, Cita comweco monga momwe wanena.
Werengani mutu wathunthu Genesis 18
Onani Genesis 18:5 nkhani