Genesis 19:13 BL92

13 popeza ife tidzaononga malo ano, cifukwa kulira kwao kwakula pamaso pa Yehova, ndipo Yehova anatitumiza ife kuti tiuononge.

Werengani mutu wathunthu Genesis 19

Onani Genesis 19:13 nkhani