17 Ndipo panali pamene anawaturutsa iwo kunja, anati, Tapulumuka ndi moyo wako; usaceuke, usakhale pacigwa pali ponse; thawira kuphiri, kuti unganyeke.
Werengani mutu wathunthu Genesis 19
Onani Genesis 19:17 nkhani