Genesis 19:20 BL92

20 taonanitu, mudzi uwu uli pafupi pothawirapo, ndipo uli wong'ono; ndithawiretu kumeneko, suli wong'ono nanga? ndipo ndidzakhala ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 19

Onani Genesis 19:20 nkhani