Genesis 20:11 BL92

11 Ndipo Abrahamu anati, Cifukwa ndinati, Pompano palibe ndithu kumuopa Mulungu, ndipo adzandipha ine cifukwa ca mkazi wanga.

Werengani mutu wathunthu Genesis 20

Onani Genesis 20:11 nkhani