Genesis 21:1 BL92

1 Ndipo Yehova anayang'anira Sara monga momwe anati, ndipo Yehova anamcitira iye monga ananena.

Werengani mutu wathunthu Genesis 21

Onani Genesis 21:1 nkhani