11 Iai, mfumu, mundimvere ine; munda ndikupatsani inu, ndi phanga liri m'menemo ndikupatsani inu, pamaso pa ana a anthu anga ndikupatsani inu; ikani wakufa wanu.
Werengani mutu wathunthu Genesis 23
Onani Genesis 23:11 nkhani