Genesis 23:15 BL92

15 Mfumu, mundimvere ine; kadziko ka mtengo wace wa masekele a siliva mazana anai, ndiko ciani pakati pa ine ndi inu? ikani wakufa wanu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 23

Onani Genesis 23:15 nkhani