8 Ndipo ananena nao, kuti, Ngati mukandibvomereza kuti ndiike wakufa wanga ndisamthirenso maso, mundimvere ine, mundinenere ine kwa Efroni mwana wace wa Zohari,
Werengani mutu wathunthu Genesis 23
Onani Genesis 23:8 nkhani