Genesis 24:11 BL92

11 Ndipo anagwaditsa ngamila zace kunja kwa mudzi, ku citsime ca madzi nthawi yamadzulo, nthawi yoturuka akazi kudzatunga madzi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:11 nkhani