Genesis 24:15 BL92

15 Ndipo panali, asanathe kunena, taonani, anaturuka Rebeka, amene anambala Betuele, mwana wamwamuna wa Milika, mkazi wa Nahori mphwace wa Abrahamu, ndi mtsuko wace paphewa pace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:15 nkhani