18 Ndipo anati, Imwa mbuyanga; nafulumira nayangata mtsuko m'manja mwace namwetsa iye.
Werengani mutu wathunthu Genesis 24
Onani Genesis 24:18 nkhani