41 ukatero udzakhala wosacimwa pa malumbiro ako, pofika iwe kwa abate anga; ndipo ngati sadzakupatsa iwe, udzakhala wosacimwa pa malumbiro ako.
Werengani mutu wathunthu Genesis 24
Onani Genesis 24:41 nkhani