Genesis 24:49 BL92

49 Tsopano, ngati mudzamcitira mbuyanga zaufulu ndi zoonadi, mundiuze, ngati iai, mundiuze; kuti ndipatukire ku dzanja lamanja kapena ku dzanja lamanzere.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:49 nkhani