59 Ndipo anamlola Rebeka mlongo wao ndi mlezi wace, amuke pamodzi ndi mnyamata wace wa Abrahamu, ndi anthu ace.
Werengani mutu wathunthu Genesis 24
Onani Genesis 24:59 nkhani