Genesis 25:34 BL92

34 Ndipo Yakobo anampatsa Esau mkate ndi mphodza zophika; ndipo iye anadya, namwa, nanyamuka, napita; comweco Esau ananyoza ukulu wace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 25

Onani Genesis 25:34 nkhani