26 Ndipo ananka kwa iye Abimeleke kucokera ku Gerari, ndi Ahuzati bwenzi lace, ndi Fikoli, kazembe wa nkhondo yace.
Werengani mutu wathunthu Genesis 26
Onani Genesis 26:26 nkhani