Genesis 26:34 BL92

34 Pamene Esau anali wa zaka makumi anai, anakwatira Yuditi mwana wamkazi wa Beeri Mhiti, ndi Basemati mwana wamkazi wa Elone Mhiti:

Werengani mutu wathunthu Genesis 26

Onani Genesis 26:34 nkhani