13 Ndipo amace anati kwa iye, Pa ine likhale temberero lako mwana wanga; koma tamvera mau anga, kazimuka kunditengera timeneto.
Werengani mutu wathunthu Genesis 27
Onani Genesis 27:13 nkhani