15 Ndipo Rebeka anatenga zobvala zokoma za Esau, mwana wace wamkuru zinali m'nyumba, nabveka nazo Yakobo mwana wace wamng'ono;
Werengani mutu wathunthu Genesis 27
Onani Genesis 27:15 nkhani