23 Ndipo sanazindikira iye, cifukwa kuti manja ace anali aubweya, onga manja a Esau mkuru wace; ndipo anamdalitsa iye.
Werengani mutu wathunthu Genesis 27
Onani Genesis 27:23 nkhani