34 Pamene Esau anamva mau a atate wace Isake, analira ndi kulira kwakukuru ndi kowawa kopambana, nati kwa atate wace, Mundidalitse ine, inenso atate wanga.
Werengani mutu wathunthu Genesis 27
Onani Genesis 27:34 nkhani