38 Ndipo Esau anati kwa atate wace, Kodi muli nao mdalitso umodzi wokha, atate wanga? Mundidalitse ine, inenso, atate wanga, Ndipo Esau anakweza mau ace nalira.
Werengani mutu wathunthu Genesis 27
Onani Genesis 27:38 nkhani