Genesis 27:5 BL92

5 Ndipo anamva Rebeka pamene Isake ananena ndi Esau mwana wace. Ndipo Esau ananka kuthengo kukasaka nyama ndi kubwera nayo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 27

Onani Genesis 27:5 nkhani