Genesis 28:18 BL92

18 Yakobo ndipo anauka m'mamawa, natenga mwala umene anaika pansi pa mutu wace, nauimiritsa, nathira mafuta pamtu pace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 28

Onani Genesis 28:18 nkhani