Genesis 28:7 BL92

7 ndiponso kuti pamene anamdalitsa iye, anamuuza iye kuti, Usatenge mkazi wa ana akazi a Kanani; ndiponso kuti Yakobo anamvera atate wace ndi amace, nanka ku Padanaramu;

Werengani mutu wathunthu Genesis 28

Onani Genesis 28:7 nkhani