9 Pamene Leya anaona kuti analeka kubala, anatenga Zilipa mdzakazi wace, nampatsa iye kwa Yakobo kuti akhale mkazi wace.
Werengani mutu wathunthu Genesis 30
Onani Genesis 30:9 nkhani