Genesis 32:17 BL92

17 Ndipo anauza wotsogolera kuti, Pamene akomana nawe mkuru wanga Esau ndi kufunsa iwe kuti, Ndiwe yani, umuka kuti? za yani zimenezi patsogolo pako?

Werengani mutu wathunthu Genesis 32

Onani Genesis 32:17 nkhani