Genesis 33:1 BL92

1 Ndipo Yakobo anatukula maso ace, taonani, anadza Esau, ndi pamodzi naye anthu mazana anai. Ndipo anagawira ana kwa Leya, ndi kwa Rakele, ndi kwa adzakazi awiri aja.

Werengani mutu wathunthu Genesis 33

Onani Genesis 33:1 nkhani