10 Ndipo mudzakhala pamodzi ndi ife, dziko lidzakhala pamaso panu; khalani m'menemo ndi kucita malonda, ndi kukhala nazo zanuzanu m'menemo.
Werengani mutu wathunthu Genesis 34
Onani Genesis 34:10 nkhani