16 pamenepo tidzakupatsani inu ana athu akazi, ndipo tidzadzitengera ana anu akazi, ndipo tidzakhala pamodzi ndi inu, ndi kukhala mtundu umodzi.
Werengani mutu wathunthu Genesis 34
Onani Genesis 34:16 nkhani