22 Anthuwo adzatiloleza ife tikhale nao anthu amodzi, pokhapo amuna onse a mwa ife adzadulidwa, monga iwo adulidwa.
Werengani mutu wathunthu Genesis 34
Onani Genesis 34:22 nkhani