3 Ndipo mtima wace unakhumba Dina mwana wace wamkazi wa Yakobo, ndipo anamkonda namwaliyo, nanena momkopa namwaliyo.
Werengani mutu wathunthu Genesis 34
Onani Genesis 34:3 nkhani