Genesis 35:11 BL92

11 Ndipo Mulungu anati kwa iye, Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse: ubale, ucuruke; mwa iwe mudzaturuka mtundu ndi gulu la mitundu, ndipo mafumu adzaturuka m'cuuno mwako;

Werengani mutu wathunthu Genesis 35

Onani Genesis 35:11 nkhani