Genesis 35:7 BL92

7 Ndipo anamanga kumeneko guwa la nsembe, Dacha pamenepo El Beteli: pakuti kumeneko Mulungu anaonekera kwa iye muja anathawa pa nkhope ya mbale wace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 35

Onani Genesis 35:7 nkhani