Genesis 36:35 BL92

35 Ndipo Husami anamwalira, ndipo Hadadi mwana wamwamuna wa Bedadi, amene anakantha Midyani m'dambo la Moabu, analamulira m'malo mwace: dzina la mudzi wace ndi Avita.

Werengani mutu wathunthu Genesis 36

Onani Genesis 36:35 nkhani