Genesis 37:3 BL92

3 Koma Israyeli anamkonda Yosefe koposa ana ace onse, pakuti anali mwana wa ukalamba wace; ndipo anamsokera iye malaya amwinjiro.

Werengani mutu wathunthu Genesis 37

Onani Genesis 37:3 nkhani