Genesis 37:32 BL92

32 natumiza malaya amwinjiro, nadza nao kwa atate ao: ndipo anati, Siwa tawatola; muzindikire tsono ngati ndi malaya a mwana wanu, kapena ndi ena.

Werengani mutu wathunthu Genesis 37

Onani Genesis 37:32 nkhani