8 Koma iye anakana, nati kwa mkazi wa mbuyace, Taonani, mbuyanga sadziwa cimene ciri ndi ine m'nyumbamu, ndipo anaika zace zonse m'manja anga;
Werengani mutu wathunthu Genesis 39
Onani Genesis 39:8 nkhani