Genesis 4:26 BL92

26 Ndiponso kwa Seti, kwa iye kunabadwamwana wamwamuna: anamucha dzina lace Enosi: pomwepo anthu anayamba kuchula dzina la Yehova.

Werengani mutu wathunthu Genesis 4

Onani Genesis 4:26 nkhani